اهل بیت ع

Ndi udindo wanji pa nthawi imene Imamu Mahadi akadali mobinsikamu ????
Ndi udindo wa inu ndi ine ndi oti I mamu Mahadi akadali mobinsika mu ndi mudziwa koma pogwilinsila ntchito mtima ndithu osati mu thupi ndithu. Chabe ndithu , komanso kuonjedzelapo nkhani ina ndi yakuti udindo wina mwa ifeyo ndi oti ndithu . kumuthandidz
Mu nkhani iyi ikutifotojodzela ndithu nkhani yopanga duwa kudzela kwa anthu , okondedwa inalipo ndithu. Komanso Imamu sajjadi adalankhula pa nkhani ndidzovomeledza kupempha mu njila anthu amenewa olemekedza wa ndithu. Monga ngati olo abale ake a nabbi
chidule cha nkhani ya umumu ndi choti pa umtsogoleri wa pambuyo pa mtumiki muhammadi kuti kodi umtsogoleri akuyenela kusankha anthu or mtumiki mwini wake mtumiki yu ? umumu zikutanthaudzanso kuti azathu asunni amati umtsogoleri ndi nthambi chabe ya chis
ZANABU ANALI akuwalimbikinsa za kupilila Azi chimwene ake Hassani ndi Hussain A.s
cholinhga chomtumidza muhammadi s. a.w ndi kudzapulumunsa wa nthu ndithu. ku makhalidwa oipa ndithu. komanso mtumiki anali ndi zipangidzo zokwanila zozapulumunsila anthu ndithudi za umzimu ndithu. komanso anali odalilika ndithu , komanso anali wa chinsadz
Abutwalibi anali munthu anali silamu ndithu, analinso omwensa anthu ku Hajj ndithu , komanso mkadzi wa Abutwalibi anali okhulupilila za chipembedzo cha Mtumiki Ibrahimu A,s ndithu , komanso Abutwalibi anali olimba mtima ndithu , sanathawe olo pang,ono p
Umu zikulongonsoledwa kuti abi twalibi ngati amapembedza mafano mu njila yobinsa chikhulupililo cha usilamu pofuna kupulumunsa mtumiki muhammadi s.a.w dithu komanso chikhulupililo chinali ngati anyamata aku mphanga amene amabinsa chikhulupilo pofuna ku
MA UMBONI AKULENSA KUPELEKA CHOLEMBELA CHOTI ALEMBE UTHENGA OMALIDZA MTUMIKI MUHAMMADI S. A.A.W. ASANAMWALIRE NDITHU.
KULENSEDWA KWA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W KUPANSIDWA CHOLEMBELA KUTI ALEMBE UTHENGA OMALIDZA ASANAMWALILE
MSOGOLERI WA PAMBUYO AMENE ANALI OYENERA NDI NDI NDANI?
Umtsogoleri wa U Mulungu mukuyang,ana kwa Mashia
UMTSOGOLERI WA MULUNGU MUKUYANG,ANA KWA MASHIA
kusegula kwa Kheibar 2
KUKUMANA KOYAMBA KUSUGULA KHEIBAR
Mapemphero amene amapemphelo mwana wa Fatima zahara.
Kugona kwa Alie A.s pa bed la Mtumiki Muhammadi s.a.w
Mu ulaliki muli kulongonsloledwa ndithu nkhani ya kuti pali anthu anthu ena
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Mulungu povumbulutsa Muhammad (s.a.w.w) kukhala Mtumiki adapereka mtendere waukulu kwa mtundu wa anthu kuti achoke mu umbuli ndi kuponderezedwa. Mtumiki ndi ntchito yake yaikulu yomwe adaigwira adakwanitsa kuchotsa anthu muzinthu zabodza, uchinyama ndikwa
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabiyyat, Wahabisim, Azodori.
Liu lotiأمّيّ muchiluya likuchokera pa mau awiri أمّ (mai) kapena أمّة (Gulu). Anthu otanthauzira Quran adati Ummiyy kutanthauza kusawerenga monga momwe adabadwira mwa mai ake ndipo sadapite kusukulu.

Pages