Kugona kwa Alie A.s pa bed la Mtumiki Muhammadi s.a.w

Kugona kwa Alie A.s pa bed la Mtumiki Muhammadi s.a.w

Ulaliki uli umu ndi woti ukupitilila nkhani yogona Alie anagona pa bedi mmalo mwa  Mtumiki Muhammadi s.a.w pamene akafuna kupanga chipongwe adani a chislamu , anthu wa adagwilidzana zomkapanga chipongwe mtumiki mu  nthawi ya usiku.    Ndiye adansankhana mmodzi mu mifuko mifuko yawo yosiyana ndithu cholinga chokamupha mtumiki  mu nthawi imodzi ndithu.

Pambuyo pake Allah adamtumidza ngero pomuudza mtumiki muhammadi adamuudza kuti asamukile ku Madinah ndithu ,koma akamasamuka amuike m,bale wake agone pa bedi pake po ndithu .agone ngati mmalo mwa iyeyo kutanthaudza apedzeke amene angalole mabvuto a mtumiki akadakumana nawo kudzipeleka ngati mwa nsembe ndithu , ndiye zimene adapanga Imamu Alie A.s.

Ndi zimene adapanga Imamu wa Mulungu yu amene Alie A.s

 

AttachmentSize
File 12207-f-chichwa.mp435.13 MB
اشتراک گذاری: 

Add new comment

Fill in the blank.