KODI MA SHIA ALI NDI MULUNGU WINA POSAKHALA MULUNGU MMODZI YU

NANGA KODI MA SHIA ALIE A.S AMATENGA KUKHALA MULUNGU KODI NDI ZOONA ?

MU ULALIKI UWU UKUTIPHUZINSA KUTI ALIE A.S SANALI MULUNGU NDITHU KOMA KUTI ANALI MA IMAMU KAPENA  MTSOGOLERI  WA MULUNGU NDITHU ,   KOMANSO  NGATI  AMAPANGA ZODABWINSA  KOMA NDI CHIFUNILO CHA CHA ALLAH NDITHU BANSI

AttachmentSize
File 12444-f-chichwa.mp460.8 MB