Abu twalibi 1

Umu zikulongonsoledwa kuti abi twalibi ngati amapembedza mafano mu njila yobinsa chikhulupililo cha usilamu pofuna kupulumunsa mtumiki muhammadi s.a.w dithu komanso chikhulupililo chinali ngati anyamata aku mphanga amene amabinsa chikhulupilo pofuna ku

Umu zikulongonsoledwa kuti abi twalibi ngati amapembedza mafano mu njila yobinsa chikhulupililo cha usilamu  pofuna kupulumunsa mtumiki muhammadi s.a.w dithu komanso  chikhulupililo chinali ngati anyamata aku mphanga amene amabinsa  chikhulupilo pofuna kupulumunsa chipembedza cha allah ndithu. abu twalibi ndi munthu mmodzi amene analela mtumiki wa allah kufikila mpaka kwa zaka 8 ndithu. funso anamulela bwanji mwa chinsoni ku machita chipembedzo chonsiyana ? amenena kuti  abutwalibi ndi kafiri  ananena bodza ndithu.

AttachmentSize
File 12184-f-chichwa.mp437.36 MB