UMTSOGOLERI MUKUYANG,ANA AKUBANJA LA MTUMIKI S.A.W

UMTSOGOLERI WA MULUNGU NDI OFUNIKA KWA ANTHU TONSEFE PENA PALIPONSE NDI NTHAWI INA ILIYONSE NDITHU. PALBE MALO AMENE ALIBE MTSOGOLERI NDITHU POPANDA MTSOGOLERI PAMAKHALA CHINSANSAW NDITHU NNAGA CHIPEMBEDZA CHA ALLAH CHIKHALE CHOPANNDA MTSOGOLERI ?