Umtsogoleri wa Mulungu mukuyang,ana Mashia

chidule cha nkhani ya umumu ndi choti pa umtsogoleri wa pambuyo pa mtumiki muhammadi kuti kodi umtsogoleri akuyenela kusankha anthu or mtumiki mwini wake mtumiki yu ? umumu zikutanthaudzanso kuti azathu asunni amati umtsogoleri ndi nthambi chabe ya chis

chidule cha nkhani ya umumu ndi choti pa umtsogoleri wa pambuyo pa mtumiki muhammadi kuti kodi umtsogoleri akuyenela kusankha anthu or  mtumiki mwini wake mtumiki yu ? umumu zikutanthaudzanso kuti azathu asunni amati umtsogoleri  ndi nthambi chabe ya chisilamu pomwe azathu achi shia amakhulupilila zoti mapata achisilamu  komanso amakhulupila nso kuti kuti  uimama akuyenera kunsankha mwiniwake allah or mtumiki muhammadi s.a.a w . pomwe azathu achisunni amakhulupilila kuti atha kunsakha anthu ngati mwa member of parliament.

AttachmentSize
File 12260-f-chichwa.mp436.82 MB