NSICHI ZA CHISILAMU

NSICHI ZA CHISILAMU

  NSICHI KWA ahal sunnat wal Jamah zilipo five ndithu komanso ku Mpatuko wa chi Shia ndi ziliponso five palibe kunsiyana ndithu . monga ngati 1 kukhulupilila  mwa Mulungu mmodzi yekha ndithu. 2 komanso kuima mapemphelo ndithu . 3 komanso  kupeleka chopeleka ngati Zakati  kwa anthu amene ali okwaninsa kupeleka chopelekacho ndithu .4 komanso Kumanga Ramadhani  ndi kupita ku Hajj ndithu . onse amene amakhulupilila za nsichi zimenedzo ndi Msilamu ndithu .

Munthu amene alibe kutulunsa chipembedzo munthu amene ali ndi mbili ngati zimenedzo ndithu. Komanso munthu amene amadzitcha kuti ndi Msilamu kuti akamuphe amene ali ndi mbili zimenedzi , olo mtumiki ndithu analibe ufulu omupha Msilamu amene anali ndi mbili zimenezi ndithu.

 

Komanso angakhalenso amene anali amvundula mmadzi amakhala ndi mtumiki alibenso ufulu owapanga zipongwe zonsiyana siyana . chinsadzo mtumiki anapangidwa zipongwe ku Twaifi komano sanangofikila kuti tikawaphe osalakwa ndithu . Tsono kwa amene mumanena kuti tidziwapha aslamu osalakwa . Chislamu chake chiti kuti ku mene adalankhula mtumiki  s.a.w.

AttachmentSize
File 12016-f-chichwa.mp436.5 MB