KUKUMANA KOYAMBA KUSUGULA KHEIBAR

KUKUMANA KOYAMBA KUSUGULA KHEIBAR

Mu ulaliki uwu  Tibva za mphabvu ya imamu Alie A.s komanso tibva zzaa kulimba mtima  kwa Alie A.s  akufotkodza nso kuti mudela mudali anthu 20000

Komanso anthu ngati   amene anali amphabvu analipo anthu okwana 2000,  

Mu dzindamu nso munali manyumba apamwamba okwana 7  komanso amene anamangidwa mwa pamwamba kuti amagwilinsila mwa chitetedzo ndithu adaniwa .

Pomaldza peni peni  Imamu Alie A.s  wayamikila Allah wake kuti Mphabvu zimene zinali mchilelodzo  mwa Allah. Sikuti zoti amakhala nadzo mphabvu mwa iye yekha n dithu.

AttachmentSize
File 12256-f-chichwa.mp430.36 MB