Kugona kwa imam Alie A.s

Mu ulaliki muli kulongonsloledwa ndithu nkhani ya kuti pali anthu anthu ena

Mu ulaliki muli kulongonsloledwa ndithu nkhani ya  kuti pali anthu anthu ena

amagulinsa umoyo wawo pofuna kukapedza mtendele wa Allah ndithu , komanso zalongonsoledwa kuti  pali anthu ena azagulinsa umoyo wao amakhalila za uthela  kuwili  ( mamu naafiqi ndithu ) ndiye anthu amene malo awo  ndi malo aku Jahannama  . zikulongosoledwa nso kuti  chipanda kuima ndi kugona  Pa Bedi  pa che mtumiki ndithu. Komanso zikulongonsoledwa pa nkhani ku qurani imanena kuti: Mulungu akumagulanso mi mtima ya wanthu kuti ikalowensedwe ku mtendele wake ndithu.

Apa ndithu zikutiudza kuti Imamu Alie amakhala okhodzeka pa chopsya china chilichonse  pomutetedza mtumiki muhammadi S.A.W

Popanda nso chitetedzo cha Allah chili apo Imamu Alie A.s anali osachita mantha ndithu koamanso anali olimba mtima ndithu posaopa wina aliyense koma Allah yekha ndithu..

AttachmentSize
File 12206-f-chichwa.mp440.68 MB