Mapemphero amene amapemphelo mwana wa Fatima zahara.

Mapemphero amene amapemphelo mwana wa Fatima zahara.

Mu ulaliki amalongosola mmene amapemphero zainabu mwana wa Fatimah zzahara , komanso amene anali mchemwali wa Imamu Hussain a.s,

Zikulongosoledwa kutinso mayi amene amakonda kupemphera kwambiri ndithu angakhalenso nthawi iina amapemphela kwambiri mu nthawi yoti watopa ndithu .

Komanso angakhalenso Imamu Hussain  adamuudza kuti ndikamwalila ndithu udzindipangila ma duwa ndikamwalilamo ndithu.

Tiyeni tibvelele limodzi ulaliki ndithu!!!!!!!!

AttachmentSize
File 12208-f-chichwa.mp434.48 MB
اشتراک گذاری: 

Add new comment

Fill in the blank.