MSOGOLERI WA PAMBUYO AMENE ANALI OYENERA NDI NDI NDANI?

MSOGOLERI WA PAMBUYO AMENE ANALI OYENERA NDI NDI NDANI?

Mu ulaliliki  uwu u ukunsiindikidza kuti kuti panali  Ma swahabah anakana kupeleka cholembela kwa Mtumiki kuti alembe uthenga omalidza kuti pambuyo aslamu asadzansochele ndithu pambuyo pomwalilla mtumikiyo ndithu. Komanso zalongonsoledwanso kuti nkhani ya Saqifah komanso nkhani ya nkhondo imene inachitika pambuyo pa mtumiki imene imatchedwa kuti  nkhondo ya Jamali ndi nkhani nso ya kuphedwa kwa Imamu Hussain A.s

.komanso zalongonsoledwanso za kusavela kwa Maswahabah kwa komanda wawo usamah bunu Zaidi ndithndi zina zotelo………

AttachmentSize
File 6361-f-chichwa.mp456.89 MB