پیامبر اسلام

 MCHISLAMU SI CHA NKHONDO AYI , MCHISILAMU NDI MTENDELE NDITHU .
NGATI PALI ANTHU AMAYAMBINSA NKHONDO MCHISILAMU KUBVALA ZA USILAMU AMENE SI ASILAMU KOMA ABVALA DZINA LA USILAMU CHIFUKWA MTUMIKI SAMAYAMBINSA NKHONDO OLO PANG,ONO POMWE NDITHU.
MLOLWA WA PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W.
UMU NKHANI YAKULA MU PHUDZILO LATHU LI NDI NKHANI YA MMLOWA MMALO WA AKUBANJA LA MTUMIKI NDITHU , NDITHU MONGA NGATI UKULONGONSOLA KUTI OYENELA KUKHALA MTSOGOLERI AKYENELA KUNKHIDWA NDI MULUNGU KAPENA NDI MTUMIKI MWINI WAKE NDITHU. PA UMBONI UWU اني جاعل
KUNSACHIMWA  KWA AKUBANJA LA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W.
MPATUKO WA CHI JAFARI A.S UMAKHULUPILILA ZOTI AMTSOGOLERI A CHIPEMBEDZO KAPENA ( ALOWA MMOLOWA A MULUNGU ) SAKUYENELA KUKHALA OPANGA ZA MACHIMO NDITHU . CHIFUKWA AKAKHALA OCHIMWA PA MANSO PA GULU SAKHALA ANTHU AZINSADZO ZABWINO NDITHU
UMUMU TIKULONGONSOLELANA NKHANI YOKHUDZA MTSOGOLERI WA PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W … KOMANSO NDI UBWINO OKHALA NDI MTSOGOLERI MU DZIKO KAPENA MU MU SOCIETY NDITHU
chidule cha nkhani ya umumu ndi choti pa umtsogoleri wa pambuyo pa mtumiki muhammadi kuti kodi umtsogoleri akuyenela kusankha anthu or mtumiki mwini wake mtumiki yu ? umumu zikutanthaudzanso kuti azathu asunni amati umtsogoleri ndi nthambi chabe ya chis
cholinhga chomtumidza muhammadi s. a.w ndi kudzapulumunsa wa nthu ndithu. ku makhalidwa oipa ndithu. komanso mtumiki anali ndi zipangidzo zokwanila zozapulumunsila anthu ndithudi za umzimu ndithu. komanso anali odalilika ndithu , komanso anali wa chinsadz
MA UMBONI AKULENSA KUPELEKA CHOLEMBELA CHOTI ALEMBE UTHENGA OMALIDZA MTUMIKI MUHAMMADI S. A.A.W. ASANAMWALIRE NDITHU.
Kugona kwa Alie A.s pa bed la Mtumiki Muhammadi s.a.w