MA UMBONI AKULENSA KUPELEKA CHOLEMBELA CHOTI ALEMBE UTHENGA OMALIDZA MTUMIKI MUHAMMADI S. A.A.W. ASANAMWALIRE NDITHU.

MA UMBONI AKULENSA KUPELEKA CHOLEMBELA CHOTI ALEMBE UTHENGA OMALIDZA MTUMIKI MUHAMMADI S. A.A.W. ASANAMWALIRE NDITHU.

zikuonekela kuti nthawi imene amalensedwa kupansidwa cholembela ena mwa ma swahabah analipo umari  r.a ndi masahabah ena  ndithu,  komanso zimene amapanga ma sahabah wa zi kunena chilungamo chake chinamkwiinsa mtumiki ndi kudandaulinsa kwambiri ndithu. potengela kuti inali mistake ya ikulu kwambiri ndithu.

   mawu amene amakonda kugwilinsila chipongwe chi ndi kunena kuti ( aaaa munsiyeni mtumiki yo matenda apengensa sakudziwa chimeneakupanga ndithu )  chimene chinali chipongwe chachikulu ndithu. )

ena mutha kumanena kuti masahabah samapanga zi ntchito zonsemphana ndi malamulo aa allah  chabwino ! munsaiwale kuti panali masahabah ena anali akambele mbele ( athila kuwili ) si onse masahabah anali opanga  za machimo ndithu . umboni ndi suratul verse 101 ndithu.

AttachmentSize
File 6369-f-chichwa.mp440.87 MB
اشتراک گذاری: 

Add new comment

Fill in the blank.