اهل بیت ع

NDI ZOTHEKANSO KUUKA PAMBUYO POTI  PA IFA NDITHU .
KWA ALLAH PALIBE CHOBVUTA KUKA KWA AKUFA CHIFUKWA UMOYO WATHU WU ULI MMANJA MWA ALLAH MWINI WAKEYO NDITHU.
CHIFUKWA ANALUDZA ALIE PA NTHAWI IMENE AMAFUNA KU MPANGA CHIPONGWE MKADZI WAKE FATIMAH ZZAHARA ?
CHIPEMBEDZO CHA CHISILAMU SICHINGAKWELE CHIFUKWA CHA LUPANGA NDITHU KOMANSO NDI NKHONDO NDITHU.
IMAMU KHUMAINI AMADZIWA ZOTI AKUBANJA LA MTUMIKI NDI APAMWAMBA KUPONSA AMTUMIKI AMENE ACHOKELA MUMA BANI ISRAEEL
NDITHU AKUBANJABA LA MTUMIKI NDI APAMWAMBA KUPONSA ATUMIKI AMA BANII ISRAEEL NDITHU
UPAMWAMBA WA IMMU ALIE A.S POYANG,ANA MA UMBONI OSIYANA SIYANA.
MUKAFUK NDU WATHU MU MCHISLAMU NDI WOTI MUNTHU AMENE ANALI OPHUDZILA IUMIPAMBUYO PA MTUMIKI WAMWLILA NDI ALIE A.S KOMANSO MUNTHU AMENE ANALI OPEDZELEKA PA CHILUNGAMO KOMANSO NDI AMENE ANALI MUNTHNU OKONDA IKUPEMPHELA KWAMBIRI NDITHU KOMANSO NDI MNTHU MMO
UPAMWAMBA WA IMMU ALIE A.S POYANG,ANA MA UMBONI OSIYANA SIYANA.
MUKAFUK NDU WATHU MU MCHISLAMU NDI WOTI MUNTHU AMENE ANALI OPHUDZILA IUMIPAMBUYO PA MTUMIKI WAMWLILA NDI ALIE A.S KOMANSO MUNTHU AMENE ANALI OPEDZELEKA PA CHILUNGAMO KOMANSO NDI AMENE ANALI MUNTHNU OKONDA IKUPEMPHELA KWAMBIRI NDITHU KOMANSO NDI MNTHU MMO
 UMTSOGOLERI MUKUYANG,ANA AKUBANJA LA MTUMIKI S.A.W
UMTSOGOLERI WA MULUNGU NDI OFUNIKA KWA ANTHU TONSEFE PENA PALIPONSE NDI NTHAWI INA ILIYONSE NDITHU. PALBE MALO AMENE ALIBE MTSOGOLERI NDITHU POPANDA MTSOGOLERI PAMAKHALA CHINSANSAW NDITHU NNAGA CHIPEMBEDZA CHA ALLAH CHIKHALE CHOPANNDA MTSOGOLERI ?
UMTSOGOLERI UKUYENELA KUNSANKHIDWA NDI MUNTHU OKONDEDWA NDI ALLAH NDITHU KOMNSO AMAKONDA ALLAH NDITHU . KOMANSO UKUYENELA KUNSANKHIDWA NDI ALLAH NDI MTUMIKI OSATI NDI ANTHU.
MGWILIDZANO WABWINO PA SOCIETY NDIN MU MCHIPEMBEDZO
MGWILIDZANO NDI WA BWINO PA DZIKO LAPANSI NDITHU. KOMANSO NDI PA GULUNSO GWILIDZANO NDI OFUNIKILA KWAMBIRI ZEDI NDITHU POPANDA NSANKHO NDITHU
 MCHISLAMU SI CHA NKHONDO AYI , MCHISILAMU NDI MTENDELE NDITHU .
NGATI PALI ANTHU AMAYAMBINSA NKHONDO MCHISILAMU KUBVALA ZA USILAMU AMENE SI ASILAMU KOMA ABVALA DZINA LA USILAMU CHIFUKWA MTUMIKI SAMAYAMBINSA NKHONDO OLO PANG,ONO POMWE NDITHU.
KUPEMPHA KWA MUNTHU ANAMWALILA KODI NDI SHIRKI KWA ALLAH
KODI MU7 DZINA LA AKUBANJA MTUMIKI NDI SHIRK KWA ALLAH KODI ? KUNENA MU CHILUNGAMO NDITHU KUTI KUPEMPHA KWA ALLAH SI KOLENSEDWA NDITHU . UMBONI NDI OTI OR ANA MNENERI YAAAQUUBI ANAPEMPHA CHIKHULULUKO KWA ABAMBO AKE AMENE ANALI YAAQUUBI NDITHU.KUTANTHAU
MALO A SAQIFAH
MALO AMENE ANANSONKHANA ZOKANSANKHANA MTSOGOLERI WA UMLOWA MMMALO NDITHU MALO MWA MTSOGOLERI AMENE AANANSANKHIDWA NDI MTUMIK MUHAMMADI S.A.A.W
KU SAQIFA KUNACHITIKA CHIYANI ?
NKHANI NDI YAKUTI PAMBUYO POTI MTUMIKI MUHAMMADI S.A.A W WAMWALILALA MAGULU AWIRI ANAKANSANKAHANA ZA UMTSOGOLERI WA MCHIPEMBEDZO PAMBUYO POTI MTUMIKI WA NSANKHA KALE NDITHU PA GHADIRI GHUMU
ZINACHITIKILA FATIMAH PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.A W
INAOTCHEDWA MNYUMBA YA ALIE A.S NDI FATIMAH ZZAHARA A.S PAMBUYO POMWALILA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.A W CHIFUKWA CHOTI ANAKA KUBVOMELEDZA ZA UMTSOGOLERI WA KHALIFA WA ABUBAKARI (R.A). FUNSO CHIFUKWA CHIYANI?
IMAMU MAHADI A.S
NKHANI YAKULA UMUMU NDI YOLONGONSOLA UMTSOGILERI WATHU CHIPEMBEDZO CHACHISILAMU CHI NDITHU WA NTHAWI INOYO PAMBUYO POTI PADUNSA AZIMTSOGOLERI A MULUNGU OCHOKELA KU BANJA LA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W IKWANA 11 . NDIYE KUTI AMENE ALIPO NTHWI INOYO NDI OMALID
MLOLWA WA PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W.
UMU NKHANI YAKULA MU PHUDZILO LATHU LI NDI NKHANI YA MMLOWA MMALO WA AKUBANJA LA MTUMIKI NDITHU , NDITHU MONGA NGATI UKULONGONSOLA KUTI OYENELA KUKHALA MTSOGOLERI AKYENELA KUNKHIDWA NDI MULUNGU KAPENA NDI MTUMIKI MWINI WAKE NDITHU. PA UMBONI UWU اني جاعل
UMTSOGOLERI PA MBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI AKUYENERA KUKHALA NDANI
UMUMU TIKULONGONSOLELANA NKHANI YOKHUDZA MTSOGOLERI WA PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W … KOMANSO NDI UBWINO OKHALA NDI MTSOGOLERI MU DZIKO KAPENA MU MU SOCIETY NDITHU.
KUNSACHIMWA KWA AKUBANJA LA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W.
MPATUKO WA CHI JAFARI A.S UMAKHULUPILILA ZOTI AMTSOGOLERI A CHIPEMBEDZO KAPENA ( ALOWA MMOLOWA A MULUNGU ) SAKUYENELA KUKHALA OPANGA ZA MACHIMO NDITHU . CHIFUKWA AKAKHALA OCHIMWA PA MANSO PA GULU SAKHALA ANTHU AZINSADZO ZABWINO NDITHU
UMUMU TIKULONGONSOLELANA NKHANI YOKHUDZA MTSOGOLERI WA PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W … KOMANSO NDI UBWINO OKHALA NDI MTSOGOLERI MU DZIKO KAPENA MU MU SOCIETY NDITHU
MLOLWA WA PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W.
NKHANI YAKULA UMUMU NDI YOLONGONSOLA UMTSOGILERI WATHU CHIPEMBEDZO CHACHISILAMU CHI NDITHU WA NTHAWI INOYO PAMBUYO POTI PADUNSA AZIMTSOGOLERI A MULUNGU OCHOKELA KU BANJA LA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W IKWANA 11 . NDIYE KUTI AMENE ALIPO NTHWI INOYO NDI OMALID

Pages