امام زمان عج

IMAMU MAHADI A.S
NKHANI YAKULA UMUMU NDI YOLONGONSOLA UMTSOGILERI WATHU CHIPEMBEDZO CHACHISILAMU CHI NDITHU WA NTHAWI INOYO PAMBUYO POTI PADUNSA AZIMTSOGOLERI A MULUNGU OCHOKELA KU BANJA LA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W IKWANA 11 . NDIYE KUTI AMENE ALIPO NTHWI INOYO NDI OMALID
MLOLWA WA PAMBUYO PA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W.
NKHANI YAKULA UMUMU NDI YOLONGONSOLA UMTSOGILERI WATHU CHIPEMBEDZO CHACHISILAMU CHI NDITHU WA NTHAWI INOYO PAMBUYO POTI PADUNSA AZIMTSOGOLERI A MULUNGU OCHOKELA KU BANJA LA MTUMIKI MUHAMMADI S.A.W IKWANA 11 . NDIYE KUTI AMENE ALIPO NTHWI INOYO NDI OMALID
Ndi udindo wanji pa nthawi imene Imamu Mahadi akadali mobinsikamu ????
Ndi udindo wa inu ndi ine ndi oti I mamu Mahadi akadali mobinsika mu ndi mudziwa koma pogwilinsila ntchito mtima ndithu osati mu thupi ndithu. Chabe ndithu , komanso kuonjedzelapo nkhani ina ndi yakuti udindo wina mwa ifeyo ndi oti ndithu . kumuthandidz
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia
Imam Mahdi (a.s) asadabwere padzakhala zinonetsero zakubwera kwake ndipo zionetsero zimenezi zili za mitundu iwiri: a- Zionetsero zakumayambiriro kwa kubwera kwake. b- Zionetsero zotsimikiza kubwera kwake ( zikaoneka zimenezo ndiye kuti nthawi yakubwera