UMTSOGOLERI WA MULUNGU MUKUYANG,ANA KWA MASHIA

UMTSOGOLERI WA MULUNGU MUKUYANG,ANA KWA MASHIA

UMU ZIKULONGONSOLEDWA KUTI IMAMU AMENE ALI OLONGONSOLA ZA MULUNGU AKUYENELA KHUKHALA OPHUDZILA KWA MBIRI . MONGA NGATI IMAmu alie  anali mpulumunsi kwa Umar pomuombola kwa zimene zimabvuta kuyankha mafunso ,monga chinsadzo Tsiku lina panali munthu waminsala  amene Anapanga chiwelewele , amene analamulidwa kuti akwapulidwe zikoti kumachita ndi wa minsala , atatulukila Imamu Alie A.s anamuongolera  Umar ku chigamulo cha munthu wa minsala yo (  kuti alibe chigamulo chifukwa wa minsala alibe chigamulo chifukwa NZERU ALIBE )

MAPETO wa minsala anapulumuka ndithu komanso anapulumuka Umar R.A  pa maphudzilo A imamu Alie A.s ndithu. 

 

AttachmentSize
File 12261-f-chichwa.mp456.61 MB