اهل بیت ع

Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Fatima ndi mwana wa Mtumiki (s.a.w.w). Iye ali maina opatsidwa (laqab) ambiri monga: Zahra, Maridhiyya, Batuli, Muhditha ...
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Fatima ndi mwana wa Mtumiki (s.a.w.w). Iye ali maina opatsidwa (laqab) ambiri monga: Zahra, Maridhiyya, Batuli, Muhditha.Tikafuna kukamba za upamwamba wake pamaso pa bambo ake (s.a.w.w) kwakwana kunena kuti:..
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Iye azamenya nkhondo ndi adani ake komanso otsutsana naye. Chifukwa choti pazapezeka magulu ena omwe sadzagwirizana ndizomwe azidzalalikira ndikuitanira iye komanso kukhazikitsa kwake chilungamo.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Mtumiki adanena kuti nthawi ya Imam Zaman umoyo wudzakhala wapamwamba kuposa nyengo zonse ndipo chuma chidzapita patsogolo komanso nthaka sidzasiya kanthu osakameretsa.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia, Shia, Shiism, chisilamu, Islam, Wahabiyyat, nkhani, Ahal bait, Wahabism, Azodori.
Pankhani yakubwera kwa Mahdi mashia ndi Ahlu sunnat ndiogwirizana maganizo angakhalenso amene sali asilamu za Imam ameneyu zidalembedwa mmabuku awo kuti kumapeto kwa dziko kudzabwera mpulumutsi.
Quran, Sunnah, Din, Religion, Wahabism, Sunni, chishia
Imam Mahdi (a.s) asadabwere padzakhala zinonetsero zakubwera kwake ndipo zionetsero zimenezi zili za mitundu iwiri: a- Zionetsero zakumayambiriro kwa kubwera kwake. b- Zionetsero zotsimikiza kubwera kwake ( zikaoneka zimenezo ndiye kuti nthawi yakubwera

Pages