Umtsogoleri wa U Mulungu mukuyang,ana kwa Mashia

Umtsogoleri wa U Mulungu mukuyang,ana kwa Mashia

Mu ulaliki ulu umu muli nkhani ya yoti munthu amene akuyenera kukhala ndi Umtsogoleri akhale ndi mbili zabwino ngati  : maphudzilo , komanso umtgoleri amansankha ndi  Mulungu komanso ndi mtumiki Muhammadi S.a.a w. komaso nkhani ya Umtsogoleri siikhudzana ndi  ukulu kapena kukhala ndi Mchuma ayi . chifukwa or nthawi ya atumiki azizikulu analipo azikulu azikulu ndi mchuma  koma Allah chifukwa mchiyani azikulu zikulu wo sadansankhe ?

Komanso mtsogoleri  wa chisilamu wa Umulungu akhale ndi mbili yothensela mabvuto aa wanthu tsiku ndi tsiku .

AttachmentSize
File 12262-f-chichwa.mp438 MB
اشتراک گذاری: 

Add new comment

Fill in the blank.