kusegula kwa Kheibar 2

kusegula kwa Kheibar 2

nkhani yakula umu mu ulaliki wu ndi yakuti mu ntahwi ya mtumikmi kunali zochitika zambiri  zina mwa zochitikadzo zinali  kusegula kheibar ( imene inali inachitika pakati pa anthu okanila kwa Allah  ndi mtumiki amene anali ma ayudah ndithu .

Komanso umu mukulongonsoledwa kuti  Imamu  Alie  A.s anali wa mphabvu kuponsa  Osatila Amtumiki muhammadi s.a.w.  ( ma sahabah).

Ndiye zafotokodzeledwanso kutinso  pa Nkhondo ya Kheibar   Ma Sahabah ena  anathawa pakufooka kwa mu mphabvbu zawo,   izizi znapanginsa kunyansidwa zimene zziznachitika kwa Masahabah zi , ndiye mmalo mwa ke ananatumidza Imamu A lie A.s kuti akalande Kheibar imene analephela kulanda ma Sahabah ndipo anapita ndithu kukalanda ndithu analandadi ndithu . anagonjensa ndithu adani achisilamu amene wa ndithu(amene anali ma ayudansi ndithu ) komanso zikukunedwanso kuti Mu ulalikimu kuti pambuyo poti wagonjensa Adani aja Mtumiki Muhammadi S.a.a.w  anampansa Munda wa Fadaki  ndithu .

AttachmentSize
File 12257-f-chichwa.mp431.2 MB