NDI MAPEMPHELO ANJI AMENE ALI APAMWAMBA OTI MUNTHU AZIGWADILA MULUNGU WAKE ?

NDI MAPEMPHELO ANJI AMENE ALI APAMWAMBA OTI MUNTHU AZIGWADILA MULUNGU WAKE ?

  KODI MUKAMAONA PANO PA DZIKO LA PANSI LINO KWA ZIMENE ADALENGA DZI BANSI MULUNGU ADANGOLENGA KUKHALA ZOPANDA NTCHITO ?

INUYO MSILAMU MZANGA MUKAMAONA NDI KUGANIDZA MODZAMA MUNTHU AMENE AMAKHALA ALIBE CHOLINGA AMATCHEDWA NDANI ?

 ndikukhulupilila amene amakhala opanda mcholinga amatchedwa kukhala wa minsala pomwe Allah ndi nzeru za mkuya kwambiri ndithu kwa china chilichonse pano pa dziko lapansi lino ndithu .

ko telo Allah sangalenge munthu pa ndi mkutumidza pano pa Dziko lapansi lino kuti azikakhala busy ndi za Dziko lapansi lino , Mulungu pa Dziko lapansi lino sanamulengele zimenedzo . anamulengela kuti azigwadila Allah yo , kuchokela mukugwadila Allah yo munthu azapansidwa mtendele pano pa Dziko lapansi lino komanso ndi tsiku la chiweludzo ndithu koamanso angakhale ndi mmandanso  inshallah ndithu.  

AttachmentSize
File 6569-f-chichwa.mp427.81 MB