Kudzinsunga kwa Mwana wa Fatimah Zzahara amene anali Zainabu A.s.

Kudzinsunga kwa Mwana wa Fatimah Zzahara amene anali Zainabu A.s.

Mu ulaliki uwu muli nkhani yoti  Zainabu anali  mzimayi mmodzi wodzunsunga ndithu .komanso zikukambidwa kuti kwa amene angakhale akudzinsunga mu thuphi lake azawelengedwa kuti ali ndi malipilo kuti ndi malipilo oponsela kwa uyo amamenya  nkhondo ya Mulungu yolimbana ndi adani achisilamu ndithu imene ili  (  nkhondo ya U Mulungu ndithu)

Zainabu zikukunedwa nso kuti nthawi imene amapangidwa zipongwe  kwa Adani achislamu zomuyalunsa kuthuphi lake kuti mwina thuphi lake amuonele anthu   koama mzimayi amene ali oyera amayensensa kuti azitchinge pogwilinsila mzanja olo nthawi ina amayensela kubinsa ndi mzanja lake la madzele pochita manyadzi mu kuyera kwa ke ,zimene zikutanthaudza kuti samalola thuphi lake kuligulinsa kwa azimuna komanso kwa anthu amene anali osayenera kumuona thupi lake ndithu.

Izizi amapanga Mzimayi ameneyo podzidziwa kuti thuphi lakelo ndi lolemekedza ndithu ,moti thuphi ndi thupi limodzi lolemekedza ndithu kwambiri . kotero sibwino  mzimayi mwa iyeyo asamadziziwe mu ulemelo wake Allah adampansa .pomangoliyanika thuphi lake kwa Azibambo amene Sali abale ake ndithu ..

Chonde  azimayi khalani odzinsungila ulemu ngati mzimayi  Zainabu  A.s   mwana wa Fatimah zzahara A.s.  

AttachmentSize
File 12209-f-chichwa.mp446.31 MB