Chiwelengero cha atsogoleri pambuyo pa mtumiki (S.A.A.W) 2

Ahalsunna akulephera kulongosola momveka bwino pokhudzana ndi Hadith yomwe mtumiki adanena kuti pambuyo pake padzabwera atsogoleri okwana khumi ndi awiri (12). Ndipo munthu akufunsa kuti kodi atsogoleri amenewa ndi ndani?

AttachmentSize
File 9bb46cc5b9c074cba1f61d66b5f8834a.mp413.83 MB