Ulemelero wa Imam Husein (A.S) Part-2

Mngelo Jibril adafika kwa mtumiki (s.a.a.w) ndipo adamusangalatsa mtumiki Muhammad (s.a.a.w) pomuwuza kuti posachedwapa mwana wako wamkazi Fatima (a.s) azakhala ndi mwana yemwe adzaphedwa ndi Ummah wako pambuyo pako.

AttachmentSize
File a43aecd08c8bcb2e0a2d5905f5b5779c.mp427.99 MB