Chilungamo ndi chiti? Part-4

Mulungu adamupatsa munthu mboni ziwiri kapena kuti atumiki awiri, Mtumiki ndi nzeru. Cholinga chomwe Mulungu adalengera zinthu ziwirizi ndi chimodzi komwe kuli kuwawongolera anthu ku chilungamo. Mwachoncho ndi zachidziwikire kuti ngakhale ndi pang’ono pomwe zinthu ziwirizi sizidzatsutsana ndipo sizingatheke kuti zitsutsane mpakana kalekale.

AttachmentSize
File 682f2e2ec4dfb1f26b7c06dc83fb50e0.mp47.21 MB