Chipembedzo cha Mulungu chiri mu nzeru zabwino ndi muchilengedwe cha Munthu

Munthu aliyense ayenera kudziwa ndi kukhulupilira za chipembedzo chabwino potsatira nzeru zake ndi chilengedwe chake. sakuyenera kukakamizidwa ndi munthu wina ayi pokhapokha maumboni kwa iye atawonekera poyera kuti chimenecho ndi chilungamo.

AttachmentSize
File 34ce3ad0a69dadfc255c0af06696b4e5.mp429.86 MB
اشتراک گذاری: 

Add new comment

Fill in the blank.