Zomwe munthu ayenera kudziwa 3

Imam mahdi (aj) ndi mtsogoleri omaliza ndipo potengera m'mene ma Hadith akunenera kuchokera kwa Asilamu onse, munthu yemwe angamwalire asakumudziwa mtsogoleri wanthawi yake ndiye kuti wamwalira ali mbuli.

AttachmentSize
File 29299222f5ede8e3ad859e72a43e21ee.mp423.38 MB