Kumudziwa Imam Sadiq (A.s) mwachidule (1)

Titha kuzindikira ulemelero wa Imam Sadiq (A.S) kudutsira mu zinthu zomwe adatisiyira ndi zomwe adalankhula pofuna kumugwira dzanja munthu ndikukamufikitsa kwa Mulungu. Monga Misbahu Alshariah pokhudzana ndi munthu yemwe akufuna kufika kwa Mulungu.

AttachmentSize
File 0293f5a8ae8865c822be2055ea39f217.mp414.42 MB
اشتراک گذاری: 

Add new comment

Fill in the blank.