Kodi Quran idasokonezedwa kapena ayi? (3)

Akumati ma Ayawa adalipo koma adachotsedwa. Kodi ma Ayawa adali pati mu Quran? Kodi kumeneku sikukhulupilira zakuti Quran idasokonezedwa popungulidwa ma Ayah ngati amenewo pakati pa Ahalsunna? Kodi izinso sizomwe zikulozera pakati pawo palinso ma umboni omwe amatsimikizira kuti Quran idasokonezedwa?

AttachmentSize
File da890e70924dd8d75ca3c5509baec622.mp420.97 MB