Kodi tidzayankha chiyani mu usiku wathu oyamba m’manda: Imam (mtsogoleri) wathu ndi ndani?-3

Imam Ali (A.S) pankhondo ya Siffin adanena kuti: أنا النبأ العظیم الذی فی اختلفتم و فی خلافتی تنازعتم “Ine ndiye nkhani yaikulu ija yomwe inu mudasemphana komanso mudakangana pokhudzana ndi ulowa m’malo wanga

AttachmentSize
File 30af126bde62e4b77cbd0f509604931e.mp428.17 MB

Add new comment