Kodi Quran idasokonezedwa kapena ayi? (2)

Choti mudziwe abale athu okondedwa, nkhani iri apa siyofuna kuwanena ma Shia kuti amakhulupilira za Quran ina ayi. Ndithudi anthu omwe amaterowo amadziwa bwino lomwe kuti Shia samakhulupilira za kusokonezeka kwa Quran ayi komanso samagwadira Ahalbait (A.S) ndinso samawafikitsa pa mlingo wa Umulungu

AttachmentSize
File 86a638b884bd6a987db6b3a75a54cd10.mp421.53 MB

Add new comment