Maina a atsogoleri (12) pambuyo pa mtumiki (S.A.A.W)

Ahalsunna akulephera kulongosola momveka bwino pokhudzana ndi Hadith yomwe mtumiki adanena kuti pambuyo pake padzabwera atsogoleri okwana khumi ndi awiri (12). Ndipo munthu akufunsa kuti kodi atsogoleri amenewa ndi ndani?

AttachmentSize
File a5b95a11c96261c7277e8af7977cfb9a.mp421.71 MB