Osafuna maphunziro ena musadagwiritse ntchito zomwe mukudziwa kale

Munthu amene angafune kudziwa zinthu zina kumachita kuti sadagwiritse ntchito zomwe akuzidziwa kale, palibe chomwe adzamuwonjezera maphunzirowo kupatulako kukanira chilungamo komanso kutalikirana ndi Mulungu. Munthu yemwe akungosonkhanitsa maphunziro osagwiritsa ntchito, idzafika nthawi yomwe adzayamba kusanza maphunziro…

AttachmentSize
File 28ca165811f15420e1fe95e567d1506e.mp424.47 MB