Kukambirana pakati pa chikhirisitu ndi chisilamu 1

Anthu akumoto azidzadandaula ndikumati: "tikadakhala tikumva zomwe anthu amanena pa njira ya chilungamo komanso tikuganiza pa zomwe zimanenedwa ndi anthu osiyana siyana, sibwenzi tiri kumoto kuno" anthu omwe amakhala onong'oneza bondo kawiri kawiri amakhala kuti adali osamva komanso osaganiza pa zomwe anthu amanena. Munthu akuyenera kumva zomwe zikunenedwa ndi ena kenako aziganize bwino ndi nzeru zake kenako ndipomwe adzatha kupeza chowonadi kuti kodi pazomwe zikulankhulidwazi zowona nanganso zabodza ndi ziti?

AttachmentSize
File f667a83c71b323ed93e662c5f395bd72.mp419.82 MB