Kulankhula kwa kholingo lodulidwa – Imam Husein (a.s) part 2

Ee inu onditsara ine! Mukamva zakuphedwa kwa munthu, ndikumbukireni ine. Ine ndi mwana wa mtumiki (mdzukulu) yemwe ndidaphedwa popanda tchimo. Ateketa ndi kulipondaponda thupi langa ndi ma Hatchi akulu akulu pambuyo pondipha. Mukadakhalapo (inu asilamu) patsiku la Ashura ndikumandiwona ine zomwe zimandichitikira. Adakana kundimvera chisoni pomwe ndidali kumupemphera madzi mwana wa miyezi 6 ndipo m'malo mwake adamuyankha mwanayu ndi mkondo omwe udazinga khosi lake. Anthuwa adavulaza mtima wa mtumiki (S.A.A.W).

AttachmentSize
File 88a6069c866f9ae5dd5465fe7fd26d39.mp416.1 MB