Ziyarat Ashura (4)

Ma Arab omwe adali munthawi ya umbuli amati ukafika mwazi wa Muharam ngati amapanga nkhondo kapena kukangana ankati nkhondo ithe kapena tiyimikire kaye chifukwa choti wafika mwezi olemekezeka… koma tikuwona kuti anthu omwe amazitcha kuti ndi asilamu komanso munthu yemwe amati ndi Khalifah wa mtumiki, adamupha Imam Husein (a.s) m'mwezi umenewu. Kodi…

AttachmentSize
File 62953f901316a61fc9f392848d650c75.mp420.02 MB