Ziyarat Ashura part 2

Quran ikupanga ziyarah powapatsa mtendere ndi kuwafunira zabwino atumiki a Mulungu nthawi zonse, koma zodandaulitsa ndipomwe tikuwapeza anthu ena omwe amazitcha kuti ndi asilamu (podziwa kuti adalamulidwa zakutsatira Quran), akumasemphana ndi mchitidwe komanso chikhalidwe cha Mulunguchi (Ziyarah) ndikumati imeneyi ndi Shirk. Kodi Quran ingatilamule kupanga Shirk?! Mulungu angatilamule kupanga Shirk?!...

AttachmentSize
File 00bf9f7f53624381545add806f3dc743.mp425.43 MB