Adaphedweranji Imam Husein (a.s) 1

Ena akumafunsa mowonetsa kutsutsa zomwe adapanga Husein (a.s) ndikumati ngati iye amadziwa kuti akaphedwa ndichifukwa chiyani adapita ku Karbala? Pomwe funso loyenera kufunsa ndi loti ngati kupita kwake kumatanthauza kuteteza Dzina la mtumiki, Chisilamu ndi kuwapulutsa asilamu kuchokera kukusochera pomwe chipembedzo chimafafanidwa, ndiye ngati amadziwa kuti zotsatira zake ndi zimenezi ndi chifukwa chiyani asapite ngakhale zidzatanthauza kuphedwa? Pomwe munthu poteteza chisilamu akuyenera kupeleka zones zomwe ali nazo ngakhale moyo wake kumene

AttachmentSize
File ae40a66340c709fd00d3452858a6d9b7.mp426.4 MB

Add new comment