Kuipa kwa miseche (2)

Miseche ndi ndiwo za agalu aku Gahena (kumoto), Munthu amene akupanga miseche ndiye kuti akudya nyama ya m’bale wake wakufa, ndipo chomwe chimadya nyama ya munthu wakufa ndi chinyama, ndiye kuti munthuyo sadzakhalanso munthu koma kuti adzakhala chinyama…

AttachmentSize
File c0468d60deca55f96ebabbf8c193f529.mp420.86 MB