Kupeleka Salam

Salam ndi chizindikiro cha kuzichepetsa ndipo ngati munthu ngati samapeleka Salam akakumana ndi asilamu anzake ndiye kuti mumtima mwake muli theka la kudzikweza. Quran ikuti ngati tikukumana ndi anthu amene ali adani athu omwe mukakumana nawo amakhala akukunyozani, m’malo mokwiya muyenera kuwapatsa Salam…

AttachmentSize
File 167d36298cb550a0fcbf3bf16a23119a.mp426.32 MB