Kodi Imam Ridha (a.s) adatisiyira chiyani? Part-1

Munthu okhulupilira akuyenera kukhala ndi mbiri komanso chikhalidwe cha Mulungu, Mtumiki ndi mtsogoleri wa nthawi yake yemwe ali osankhidwa ndi Mulungu. Chikhalidwe cha Mulungu ndi kubisa zoyipa za ena. Chikhalidwe cha mtumiki ndi kukhala bwino ndi anthu komwe kuli kuwakhululukira pazomwe akupanga ndipo chikhalidwe cha mtsogoleri wake osankhidwa ndi Mulungu pambuyo pa mtumiki, ndiko kupilira pa zovuta zonse zomwe angakumane nazo.

AttachmentSize
File a18223b57365629d1cd9a6c0a90ff48d.mp425.85 MB