Ena mwa mawu a Imam Ridha (A.S) ndi chikhalidwe chake

Munthu sakuyenera kumangolankhula zinthu zopanda phindu, dziwani kuti chete amabweretsa chikondi pakati pa anthu… Sitikuyenera kusankha ndikupatulana pakati pathu chifukwa chakusiyana mitundu, udindo ndi… sitikuyenera kusiyanitsa pakati pathu. Munthu yemwe angapereke Salamu kwa munthu osauka mosiyana ndimomwe angapelekere kwa munthu olemera, adzakumana ndi Mulungu ali omukwiyira. Tonsefe bambo komanso mayi athu ndi amodzi ndipo chomwe chidzamupambanitsa munthu ndi ntchito zake.

AttachmentSize
File 85cc2ebee54ea92f21e7b065430553a7.mp418.71 MB