Zizindikiro zakubwera kwa mpulutsi

Zina mwa zizindikiro zakubwera kwa mpulumutsi ndi izi; nkhondo yofira komwe kuli kuphedwa kudutsira muzida zosiyana siyana pomwe magazi a anthu akukhetsedwa, nkhondo yoyera komwe kuli kumwalira chifukwa chamatenda osiyana siyana komanso achilendo, kukangana m'mizikiti, tchimo lidzakhala lophweka ndipo anthu azidzawona ngati sitchimo, kukhala ndi umoyo ochepa, anthu azidzatuluka muchipembedzo chawo kupita ku chipembedzo china mosavuta, kupititsa patsogolo zaka zokwatira ndikuchepetsa zaka zopangira machimo monga chiwelewere kudutsira mukuwaletsa kukwatira anyamata komanso atsikana nthawi yokwatira itawakwanira…

AttachmentSize
File e1b83989b8851b578f51f26b756c9dbc.mp443.15 MB