Mwezi wa Ramadhan- 2

Mzimu wathu chifukwa chakudya kwambiri umakhala thupi – kutanthauza kuti mzimu omwe udali opepuka komanso ofewa, umalemera mwachoncho siungathe kuwuluka komanso siungathe kupanga ntchito zake moyenera – ndipo thupi la munthu chifukwa chakudya pang’ono limakhala mzimu

AttachmentSize
File 16e9956d0a9de49c0e24bcb9d86d3883.mp429.53 MB