Chiwelengero cha atsogoleri pambuyo pa mtumiki (S.A.A.W)

Ahalsunna akulephera kulongosola momveka bwino pokhudzana ndi Hadith yomwe mtumiki adanena kuti pambuyo pake padzabwera atsogoleri okwana khumi ndi awiri (12). Ndipo munthu akufunsa kuti kodi atsogoleri amenewa ndi ndani?

AttachmentSize
File 2b1579f450b4f4d0def079491a39499c.mp413.86 MB