Malamulo a Chipembedzo Ndi maganizo a munthu

Munthu chifukwa chakukhala kwake Muqallid, sakuyenera kuwonjezera maganizo ake pa malamulo a Mulungu ndi Mtumiki wake, popungula kapena kuwonjezera. Chifukwa akamati kapolo ndi munthu yemwe akuvomereza chilamulo cha Mulungu ndi mtumiki wake popanda kupungula kapena kuwonjezera. Kuyika maganizo pa malamulo a Mulungu umenewo ndi umulungu osati ukapolo ayi zomwe zili zolakwika.

AttachmentSize
File d6cc5abec10dff581de49feb432d1999.mp49.37 MB

Add new comment