Mayi Maria (S.A) mu Quran

Quran ikulongosola kwambiri upamwamba wa Mayi Maria (S.A) kuposa Bible. Kupezeka kwa Mayi Maria kukumudabwitsa mtumiki wa nthawi yake Zakaria (A.S). Yesu (A.S) akupanga zinthu zodabwitsa mumphamvu ya Mulungu.

AttachmentSize
File cfa8f94000113c73a28926919c98b723.mp436.59 MB

Add new comment