Kusankhidwa kwa Ali (A.S) kukhala mtsogoleri wa Asilamu

Mabukhu a anzathu okondedwa Ahalsunna omwe ali m\'musiwa,akutsimikizira za kusankhidwa kwa Ali Ibn Abi Talib (a.s) ndi mtumiki kukhala mtsogoleri wa asilamu pambuyo pa mtumiki osati munthu wina ayi: Sahih Tirmidhiy/ volume 2/ page 298, Sunan Ibn Majah/ Volume 1/ page 43 Bab Fadhaail Ali (a.s) Hadith 16, Musnad Ahman Ibn Hambal/ volume 1/ page 297 ndi mabukhu ena.

AttachmentSize
File 3e8b73f5ffede82880078c52d5daf70d.mp418.04 MB

Add new comment