Tawassul 2

Hadithiyi ndiyoti munthu wina osaona adabwera kwa Mtumiki (s.a.w.w) ndikumupempha kuti ampempherere kuti akhale bwino, Mtumiki adamuwuza kuti achite udhu mosamala kenako apemphere marakat awiri kenako apemphe ndi pempho kenako adakhala bwino.

AttachmentSize
File d48944c53a292c313eccdf857649f27e.mp420.53 MB