Imam Husain (a.s) part 15

Imam Husain (a.s) pa 2 Muharram 61 hijri adafika pa Karbala. Imam Husain adalamula anthu ake kuti aime pamalopa ndipo akhale chifukwa ndi malo omwe iye amadziwa kuti amenyera nkhondo gulu la Yazid.Ndipo adati
اللهم اني أعوذ بك من الكرب والبلاء

AttachmentSize
File e418b92efbccd10e833022dd372d732b.mp411.63 MB