Utumiki: Part 16

Mukukambirana kwadutsa tidanena kuti M’busa wina otchedwa Buhaira atamuona Mtumiki adawauze abambo ake akulu Abu Twalib kuti ayenera kumusamala iye chifukwa choti adzakhala Mtumiki wa Mulungu ndiye adani aMulungu akamuona amuchita chiwembu.

AttachmentSize
File a198b4e65c3595e8a429268d438378f4.mp431.78 MB